Uleke kumangomwa madzi okha, koma uzimwako vinyo pangʼono chifukwa cha vuto lako la mʼmimba ndi kudwala kwako kwa pafupipafupi.
1 Timoteyo 5:23
Uthenga wa Paulo kwa Timoteo.. ife ndi ndani.
15
Lero atatiwerutse ndi a Microsoft wa..
BREAKING: Hundreds of thousands of users around the world are still affected by the global outage at Microsoft, affecting its Outlook, Teams, Copilot and 365 services.
Follow the latest updates 🔗 trib.al/4O4X5hZ
📺 Sky 501, Virgin 602, Freeview 233 and YouTube
1
1
200
Basi ine busy minding my business, then out of nowhere my brain goes
🎶 Ungovomereza unaduka iwe, pangapa suza.....😭😂😂
This song eeeh😭
17
Ine nde sinayerekeze mkuvayako komwe.. mxii
30' Goal Alert!
Blue Eagles 2-0 Mighty Wanderers
Tonic Viyuyi⚽️
#442Malawi
1
52
Pa ma player amene mukunena kuti afa lero.. ineyo ndekuti mungathe kuonjezerapo, Pali ineyo komanso nzanga, ndekuti pa ma player 11 aja, lero muzinena kuti tilipo anthu 13.. Ineyo ndafa nawo
23
Joker
#Update
Silver Strikers winger, Zebron Kalima, has been named as the club's player of the month of August.
In August Kalima scored twice in a 3-0 victory against Ekhaya, where he was awarded as the man-of-the-match.
29
Aaah Mjojo..
📍 Zomba Stadium
Masters FC head coach Peter Mponda reaction after receiving a red card. #442Malawi #FdhBankPremiership
43
Tapitani uko.. nde mwamuphoda ndani wanuyo??? Lero simukugona N'town
FULL-TIME
We suffer a heavy defeat in Blantyre at Mpira Stadium.
FCB Nyasa Big Bullets 5-0 Silver Strikers
🎶Tiadode Tiadode tikamaliza tiaphode, pamapeto akhale ma Banker!!🎶
#SilverStrikersFC #TheCentralBankers #AgonaNtown #UmodziUmodzi #HallaMaBanker #LuthandoHoldings #MorningDew #CPInvestments #BlueWaves #PinnacleFinancialServices #Betway
1
75






















