Kulipo kumati president Ali pakati pathu not knowing akucheza ndi achina Mose,Yobu ndi Eliya kumwambako
1
18
Anangoyenela kumapangila delete verse, nanga nyimbo zitatu zonse kumangoti "tsiku Lina angongole azandikanganila"
13
Chat with me let's talk | Looking for interesting conversations, friendship and good vibes? Let's connect! I enjoy meeting new people, sharing experiences and having meaningful conversations. Come say hello! 😊 | Chat $30.00 Flat Rate premium.chat/Kenziemw11/1132…
42
Tikakupatsani lift osamatifunsa mtengo omwe tinagulira galimotoyo, mutha kufunsa online ma prices wo
1
20
This year I learnt a very good lesson when it comes to buying a car. Never buy a second hand car and don't involve agents
1
40
I was reading this while sipping juice mpaka ndatsamwidwa, local master mwana waku Bangwe ngati uyu? Let's be realistic and fair at the same time, when it comes to local sound no one comes close to Gibo pearson.
Kuno nkumbali akulu akulu, this kid, Kineo alandire ulemu wake. Since he switched to a solo career and the local sound, mwanayu wapanga influence a new generation of artists who are now also doing local music. Now tikamayenda paliponse tikumva mafana akuyimba nyimbo za lokolo zeni zeni.
Poyamba tu sizinali mu fashion zimenezi, oyimba wa lokolo amaoneka ngati osalira. That's why I call him The Local Master. Dolo kwambiri 🔥🔥🔥
Vote for him Best Local Act at Maso Awards : maso-awards.live/vote
119
In companies it's always this mf old folks hating on young lads, usagule nsapato ya new one, HR wayambapo ma silent investigations😂
14















