Akometsi (@akometsimw) header
Akometsi (@akometsimw) profile picture

We promote brands, entertain people and exaggerate issues. No sad moments here.

Malawi
Joined January 2020
Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)Photo by Akometsi (@akometsimw)
Sky@10: Ku BICC kuno amene sanatchene ndi Bensam yekha eeh anthu awusosola ulusi🔥🔥🔥 Kodi inu sanakuyitaneni?
1
155
Kuno nde anachita kumuuza kuti nyangwita zako umavala zija kunoko ayi ndipo Kell Kay wamvera. Muombeleni mmanja mwamuna wa Tamanda watchena 👏🏾 Sky@10
3
372
Koma Gwamba watchena 👏🏼👏🏼 Zikuchitika ku BICC komwe Sky Energy ikukondwelera zaka 10. Tayamikirani watchena uyu.
5
360
Sky@10: Sitikudziwa kuti ndi chani kweni kweni koma kuno ku BICC kukuchitika zinthu zomwe nafenso zatipatsa chidwi. Yathu ija, tikhalanso pompano kuwatapa mkamwa, kupeza ma mistake komanso kukokomeza zomwe zizichitikazo. Tava kununkhila zakudya ndi zakumwa. Achina Gwamba, Namadingo, Teddy Makadi, Praise Umali, Kell Kay akhalanso pompano akuti.
3
315
Zayambika ndipo kwachemaratu 🔥🔥🔥🙌🏾 Sopano Zeze watulutsa list yoyamba ya oimba 4, omwe akapange nawo perform ku Concert yake 'Tigona Panja' 🔥 Wayamba ndi Crispy Malawi, Driemo, Lady Aika ndi Skeffa Chimoto 🔥 Ndiye paja ma ticket ayambira K10,000. Ndipo ma ticket awawa akutha mawa kwinako adhula, guliranitu nthawi yabwino. Linkie 🔥
2
3
1
47
2,055
KODI MUMADZIWA ? Zeze yemwe waonekera kwambiri as Amapiano Artist kwa zaka 4 zimenezi komano watulutsa kale ma hit songs okwana 50 ? Just imagine🙌🏾 Zeze's Top 50 songs 1. Ndilira Mumvula ft. Yo Maps, HarryCane & Leumas 2. Kusangalala (Acoustic version) 3. Achisale ft. LeuMas, Nae Rae 4. Alamu Anu ft. NyasaPiano 5. Vula Malaya ft. Malimba Music, Leumas 6. Zonsezi Ndi Zeze 7. Mavuto ft. XDuppy, LeuMas 8. Chule ft. Afana Ceez, Tuno, Leumas, Vj Ice 9. Ndathela Pano 10. Maluzi ft. LeuMas, Amfumu Collins Bandawe 11. Mphaka ft. LeuMas, Achina Ghatta Ase, Richard Billy & Dj Drew 12. Mbama ft. LeuMas 13. Mvetsela ft. Temwah 14. Zalowa ft. Leumas, Yanos Central 15. Ndavomela ft. Don Bunji 16. Taima ft. Leumas 17. Lero ft. The Daredevilz 18. Ndamva 19. Kagwele Uko ft. Leumas, Hayz Emgola 20. Ukuzatani? ft. Leumas, Imnotsteelo, Koollay 21. Zowawa ft. Leumas 22. HEY YOU SIBUSISO ft. Dj Maphorisa, Vulela 2, Myztro, Mlusician, Debow Taliana 23. Ndamutuluka ft. LeuMas 24. Lero Zogona ayi ft. Leumas 25. Yemweyo ft. LeuMas, Zani Challe 26. Please Don't Judge Me 27. Thupi Lako ft. LeuMas, Hayze Engola 28. Azandikanganila ft. Leumas 29. Thank You ft. Leumas, VJ Ice & Dj Drew 30. Vuto Ndichani ft. Temwah 31. Sindimazitengela ft. LeuMas 32. Tipalamulapo Pano ft. LeuMas 33. Njoka 34. Asandidutse ft. LeuMas 35. Mkazi Mbambande ft. Leumas 36. Mowa Wadzulo ft. Leumas, Black Don & Siirprincey 37. 6-2-6 ft. Temwah 38. Ndabalalika ft. Vj Ice 39. Monday to Sunday ft. Leumas 40. Kale ft. Temwah 41. Ndasangalala with Way2Savage, Joe ikon 42. Ku mowa with Charisma 43. Anzanu with Kineo, Aidfest Madness 44. Chete with Malinga Mafia 45. Simmene kuliri with Deo Cruger 46. Ma set with Jain Cactus, Leumas, Durk 47. Limodzi with Joe ikon 48. Kadigong with Sho Madjozi, Tiwa Savage 49. Feli with Naerae & Leumas 50. Kwayipa with Fada Moti Kuti muonetsetse nyimbo zonsezi Ghetto imazidziwa, ndipo imaimba nawo palipose. Pakuti nyimbo zake imazikonda kwambiri ndi Ghetto, ndichifukwa chakeso waiganizira Ghetto yo, ndipo ticket yake yayambira 10K 👏🏾 Ndiye ngati kuma show aanthu ena amaimba mpakana mbembembe, ndiye ku concert yakeyi 'Tigona Panja' akaimba nyimbo 50 zonsezi ikatha liti ? Yangoyeneradi, kukayamba pa 31 Zezember mpakana 2027 iyi coz no ! Zeze yu anadza 🔥 Tiyeni ukuku tikasangalale, ma ticket a 10K akutha mawa, zungufunika kuguliratu 🔥👏🏾
3
16
1,256
Chikayamba kumene umaona ngt vuto ndamene anasiyana nayeyo 😂🙌 🔨
1
2
346
Bwanji inuyo muli ndi phone number ya Ex wanu ?
417
Oimba monga Lawi, sapezekapezeka ma show, komano akapezeka ? Umadziwa kuti apa ndimvere nyimbo ndima performance abwino ! Kotero, pitani mukamve kukoma ndi Lawi mawa, ku Rhythms & Soul from 2pm mpakana 11pm, zonse zikuchitikira ku The ROAD TRIP🔥
116
Congratulations to the 100 people who have advanced to the next stage in the Young Builders Challenge ya ku Paul Katema Foundation. Pa anthu 100 amenewa, anthu 10 ndi amene atalandire ma 3 million kwacha each kuti apangile ma business awo. The List: 1. Enoch Emmanuel Mvula — Zomba 2. Amos Mosoulin Mkambeni — Zomba 3. Tatenda Patricia Chiuye — Lilongwe 4. Susan Maziya — Dowa 5. Pegjoy Mponda — Lilongwe 6. Michael Chikumbutso — Kasungu 7. Amanda Chingoni — Lilongwe 8. Precious Valiant Mkwapatira — Lilongwe 9. Enerst Mthethwa — Mchinji 10. Stanley Oscar Mkandawire — Mzimba 11. Dominic Macdonald Mpakiza — Kasungu 12. Vanessa Mbemba — Mulanje 13. Emmanuel Thungula — Lilongwe 14. Mphatso Chikwanda — Zomba 15. Emmanuel Gerald — Lilongwe 16. Vanessa Zamadunga — Lilongwe 17. Franklin Msofi — Zomba 18. Friday Kalonga — Blantyre 19. Deinoh Spencer Tembo — Blantyre 20. Emmanuel Dzungu — Dowa 21. Miracle Maloya — Balaka 22. Prince Kabaghe Banda — Zomba 23. Madalitso Phiri — Mzimba 24. Favour Mlowoka — Lilongwe 25. Herbert Mkwinja — Lilongwe 26. Bright Selemani — Mzimba 27. Mercy Bulla — Mchinji 28. Kizito Witmos — Mangochi 29. Donita Moyo — Mzimba 30. Patricia Kauteka — Lilongwe 31. Hudson Mwangalika — Zomba 32. Innocent Maweta — Lilongwe 33. Henry Noah — Dedza 34. Jonathan Bakali Jr — Kasungu 35. Patrick Sadimba — Blantyre 36. Bright Tsoka — Mangochi 37. Chiyanjano Lifesa — Lilongwe 38. Stanley Ngozo Makala — Lilongwe 39. Peter Tembo — Blantyre 40. Fatsani Blakjak Che Kalonda — Blantyre 41. Cathreen Chalemba — Mchinji 42. Andrew Makoloni Petro — Dedza 43. Richard Munthali — Mzimba 44. Chimwemwe Suya — Lilongwe 45. Freedom Phambana — Blantyre 46. Victor Kamputa — Salima 47. Lidess Kadzidzi — Lilongwe 48. Emmanuel Likonde — Mangochi 49. Gareta Chisomo Maureen — Lilongwe 50. Chinoko Ngulube — Mzimba 51. Chayamba Jonas — Blantyre 52. Sir Godfrey Malata — Lilongwe 53. Collins Mwale — Lilongwe 54. Annie Zinyongo — Lilongwe 55. Donalisa Pawindo — Lilongwe 56. Mark Christopher Pakanati — Chiradzulu 57. Chikondi Kalaliki — Blantyre 58. Mphatso Finius — Blantyre 59. Treaser Mkwezalamba — Ntchisi 60. Patrick Jailosi — Lilongwe 61. Brave Nthakomwa — Lilongwe 62. Gift Jere — Mzimba 63. Fortune Rocio Baluwa — Lilongwe 64. Victoria Chifundo Kalebe — Mchinji 65. Brenda M. Banda — Lilongwe 66. Laurence Kadzamira — Lilongwe 67. Ganizani Msole — Blantyre 68. Nellie Ndalama — Lilongwe 69. Precious London — Ntcheu 70. Mfundo Khumalo — Balaka 71. Darlington Dick — Lilongwe 72. Talandira Phiri — Mzimba 73. Collins Chisenga — Blantyre 74. Arthur Soza — Lilongwe 75. Gift Musaya — Salima 76. Takondwa Kanyama — Lilongwe 77. Gift Sambiri — Ntcheu 78. Dumisan Kachembere — Mulanje 79. Aaron Malema — Mzimba 80. Patrick — Blantyre 81. Vincent Macadams Chiumia — Lilongwe 82. Thomas Nyirongo — Nkhata Bay 83. Christopher Trick Nkhata — Mzimba 84. Innocent K Justin — Lilongwe 85. Mphatso Rodgers — Mchinji 86. Atanie Nyambi — Lilongwe 87. Awema Kaminyu — Blantyre 88. Mphatso Hassan — Lilongwe 89. Lonely Makata — Lilongwe 90. Boaz Kambale — Lilongwe 91. Precious Nkhata — Blantyre 92. Alinane Gerald Maluwa — Dedza 93. Ezekiel James Chiwenkha — Lilongwe 94. Dorothy Sumaili — Kasungu 95. Wickess Davie Banda — Blantyre 96. Nithaar Kaisi — Thyolo 97. Leonard Juma — Salima 98. John Lloyd Makhuwira — Dedza 99. Tawina Mbeza — Lilongwe 100. Victory Pingasa — Blantyre Kwa amene simuli pa list, ndinu ma Builder anzathu. Mkokomo ndi wa tonse. Tiyeni tiwalimbikitse anzathu pamene akupita ku gawo lotsatira. 📷📷 Proudly a Builder. Tigonjetse. #MkokomoWachinyamata #YoungBuildersChallengeSeason2 #MauPangonoNtchitoPatsogolo #ProudlyABuilder #BuildersWillRise #LackOfOpportunityIsTheEnemy #Tigonjetse
187
Chaka chino ayimyamula kwambiri Malawi awiliwa. Driemo akuswa bwino ku Zambia ndi Namibia uku Zeze akulowa mkati mweni mweni mwa South Africa.
7
452
Mpakana kunja kwada? E eh tumizani!
18
1,881
Ronaldo waswa Hat-trick uku kumupangitsa kufika 985 goals, zangotsala 15 kuti afika 1000
1
4
188
Akukana kundigulira ticket ya K10,000 yaku concert ya Zeze, after zinthu zake zitakhalira manomu, is this slime not cheating on me ? Therapy Thursday on Akometsi Akometsi bhobho ? Kunonso bhobho. Ndine Tasha ndimakhala ku Area 25. am dating slime winawake koma ndikamunthu kosayamika saname ! Kamfiti. Inuyo mutalengeza kuti Ticket ku show ya Zeze yayambira 10 Sau, ndipo zitha pa 31 October, ine ndati mwayi koma uyu, then kenaka nathamangira kwawo kwa SLiME yu Then kenako kuja nangofikira kumuuze amvule, kenako kanthu kakeko nakaika mkamwamu, then kenaka natsikira kumunsiku, sanasheveso mpakana ma ujeni ake anandikanilira mano ! Nachita kuwasolola ndimanja pa from camera ya phone. komabe then kenaka zakezo anapangira nkamwamu. Then kenaka ndati ndamuvetsa mtedza, now ndimupephe andigulire ticket ija ? Koma kuti ? eti akukana kugula ticket ya 10 sau yeniyeni kuti tikagone panja tonse limodzi pa 31 Zezember chosecho ndamuuza ukatha mwezi uno pa 31 Ticket ija ifika 20, kwinako 50 sau Inu eti munthu osasamala kuti ndamuyamwayamwa ndipo ntchere wa zinthu zakezo ukumvekabe mkamwa mwangamu ? Then kenaka, ineyo eti nduganiza kuti uyuyu akakhala ndi mkazi wina paja amuna ndima bat**re awiri olendewera. Nanga ngati sakakhala ndi ine pa 31 Zezember akakhala ndi ndaa ?? Ndipo azizatani ? Sindimafuna kutukwana Akome, komano Slime Gang wakwa cent ndiwe ba***re la mano kunsi wamva !
2
196
Kulemera kwadya wani pa Town THERAPY THURSDAY ON AKOMETSI Akometsi ine ndikulemba ngati concerned citizen eeeeh Amalawi tikuphana kwambiri ndi mitengo ya zinthu. Anthu ambiri akuba kwambiri ndipo motengo ya chilungamo ikuoneka pano anthu anasiya kalekale. Mtengo wa mwado mma boutique mu eeeeh bola kumayenda changing shuwa. Ine ndazizimuka akuti mwado 300k nanga kuti ukavala udzimva kukoma ? Imagine akometsi nthambo kapena kuti zingwe za nsapato zomwezi akuti imodzi 15k, uwuw ndi mtengo wamu Boutique ndipo katundu yemweyi ku Kaunjika ukamupeza pa 1.5k basi. Ndiye anthu awa ama boutique nthawi zambiri amakhala akugona pama tiles kuseli kwa counter kuja kuli kusowa ma customer. Inde rent mmalipira yodula koma eeeeh mitengo mukumakunga udyo. Akometsi anthu ambiriwq nde akumakhala atenga Bello shit kungosita basi, umva taking orders ndipita ku Dubai next week. Ku Dubai anapita kamodzi ndi zovala zambiri mkungpjambulitza zithuz zambirmbiri angosintha kuti akalengeza kuti akupita ndekut awonetse zobvala zina basi. Mitengo sikuyenda bwino ayi eeeish ine pano ndizingogula bello ndipo awa atsikana ama boutique ndiwafunira ma tulo abwino a daily kuseli kwa counter zikomo. Photo Disclaimer: This is an AI-generated illustration photo. Any resemblance to actual persons is entirely coincidental.
1
3
1,730
Mvula aliyese akuyiwona THERAPY THURSDAY ON AKOMETSI Nyengo ikupereka ndithu ma signs and warnings ⚠️. Nthawi yolima yakwana ndithu apa. Ndiye pali mabwana ena akamcheza ndi anzawo amadzimva kuti ife chakudya timachita kugula, ali mimba kuno kunjoya mma 49 ndikuma Namiwawa. Anthu awa amakhala atambwali kwambiri ndipo samafuna kupita kumudzi ayi maka nthawi yolima chonchi. Iwowa amadikira nthawi yokolora ndiye kuyendera achibale onse akuchimuna ndi akuchikazi kupitisa soap wa Azamu ndi sugar 6 basi. Akatelo anthu akumudzi agundike kuperekq matumba a mtedza ndi chimanga kwa Amkolo aku Town. Izi chaka chino ayi, mabwana ku Town ko aliyese akalime. Ine Gong'o kuno ku Mtunthama kasungu ndikuimira anthu onse akumudzi, chaka chino aliyese alime yekha ndipo pasapezeke onamiza azake kuti azagula chonsecho amangobweresa azamu 7 kumudzi kenaka anthu amupase chimanga. Ndangokhala oyankhulira amphawi chabe, ine ndilibe abale ku Town 😂😂😂🙌. Nyengo iyi ma warning yafakq ndithu ulesi ayi, mabingu ndi ziphaliwali ndi zomwe zayambazi. Abwana zalimeni chaka chino palibe nyasi ayi mxxxiew, mabwana onunkha pakhosi ofuna kufinya amphawi kumudzi.
2
228
Kumbucha ndiye ngati Vinyo waku mwamba THERAPY THURSDAY ON AKOMETSI Akometsi moyo penapake sukuyenda mwa fair ayi. Abusa athu nde sunday iliyonse kulalila zonyoza mowa komaso kuipa kwa mowa. Koma kaya mowa unalakwa chani chifukwa tu paja mwana wake wa Mulungu ku Ukwati waku Kana anati "dzadzani mbiya izi ndi madzi" ndipo posakhalisa anasandusa Vinyo pamenepaja. Nanga ukanakhala mowa ndi oipa bwezi atasandusa? Koma abusa athu simomwe anyozera chakumwa chofumira mu mphesa, mwina ife uthenga sitimaumva bwino. Koma china chomwe chandizizimusa ndochoti ndapanga observe kuti uyu munthu wa chauta akumamwa kambiri kumbucha ndipo kumbucha alcohol percentage ndi 0.5-4.5% kuphana ndi kuchekuche. Ndiye apapa mwati abusawa samamwa mowa iwowo? Nduona ngati akuchulusa kutikhomelera kuti azinjoyq okha basi. Ndinali kwawo dzana koma kuona mu bin mabotolo olo 40 kudusa a kumbucha, chithuzi ndatumizacho ndi cha mu galimoto mwawo mabotolo a Mpesa, mdala uyu akunjoya ndipo ine ndaona kuti mowa ndisasiye ndizimwabe basi tikaone kumwamba komko apa.
4
297
Sindimva Kukoma kulikose koma ma Ex amati ndine Okoma modabwitsa THERAPY THURSDAY ON AKOMETSI Hi akometsi ngati kuli kotheka mundipangireko post nkhani yanga, Ndine mtsikana wazaka 21 km akometsi zogonanazi nde sizimandiwaza sindidziwa ngati lili vuto, Ndimadabwa athu amachita kuyamikira km ineo nde mmm ayi palibe chomwe ndimavapo mpaka ng'ono wanga anandiposa Ali ndi mimba apapa komatu ine ayi zibwezi nde zimangotha fukwa ine ndimakwanitsa kukhala bhob no feelings km nanga nzangayo?? Nkhani ndiyoti pali mamuna amene wapilira nane afuna andikwatire km ineo sundufuna abale kd sivuto km ilili kapena ndimayenera kukhala sisterie💔 Nditani ine ex wanga anandikakamira nkutopa ati am very sweet km ine nde sivapo Kathu, olo boyfriend wanga afuna andikwatireyu amati ndimakoma km ineo sindimva kukomako💔 Tafusan ma fans anu ngati lili vuto kapena alipo zimamuchitikiraso izi nanga anathana nazo bwanj? Coz ndukula muthunetu😂 ndipo ma one mmusimu alimo ndithu koma vuto zinthu zija sizindisangalasa nde ku banjako mzikataniko? Image disclaimer: we are not in any contract with the owners of the product, it has been obtained from the internet.
2
173
Tonse kwa lero ndi mawa ndife ma lecturer THERAPY THURSDAY ON AKOMETSI Akometsi FDH nayo kuti Khaaaaaaaa khaaaa ma 280k awa. Izizi ma peri sangazimvetse. Pa peripo mwina ndalemekeza ndunena anthu amene sanapiteko ku public university chifukwa aku Private wa nawoso ndi ma peri a hybrid. Ife apa ma upkeep alowa, kutsimikiza ndithu kuti momwe salary ya ma professor apano pa CHANCO ikulowa nafeso zathu zangenamo Akometsi. Lero ndi mawa ku mixed lecturer akaitanisa mowa 4 ife tizitenga 6. Ndipo ma lecturer nawoso adziwe zotia class asayelekeze kubweresa ma makeup, ife tili busy kudya ndalama. Ndalama iyi ndiyambiri siyofunika kupita nayo kumudzi atha kukatilodza nayo, atha kuwona ngati talemera. Mupange post mudyapo ka 30k kokha, Ine ndi Rajab Nyibesa, ndalama zatiyamba dala. Izi ndi ndalama zomwe boma limagawira ana a nzeru mma public university kuti amwereko mowa akamaliza kuwerenga. Ndalama izi ndi zoti umangozindikira zatha komabe umakhala wanjoya ndithu kwa nthawi imeneyo. Izotu ma peri ndi ma peri a hybrid aziona ngati tikukokomeza koma ayi ndithu ndimomwe zilili ife ana a nzeru kusililitsa eeeish. Kaya akuti Loans board yayamba kuvuta kuti anthu azibweza zimenezo ndizawo ndipo tizaziona mtsogolo mu koma for now ife tikunjoya ndithu. Image Disclaimer: not in any contract with the company just used for awareness sake.
2
363