Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98) profile picture
Joined March 2024
Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)Photo by Rejected handsome ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ผ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฆ (@omex98)
I THINK WANKULUDI NDIMULUNGU, THE WAY HE IS FUCKIN THAT GRANNY IS SOMETHING ELSE
183
Misonkho ija osazaiphweketsa munthu akamadya amanenepa nayo, tawaoneni makosanawa ali ku opposition anali owonda ingakhale anali ndi ndalama kale koma kungolowaa mu bomamu achita kudumtukiratu, iii koma msonkho iwe๐Ÿ˜ฎโ€๐Ÿ’จ
3
3
1
26
1,166
Kodi posinthira ma settings ku twitter kuno kuti ma videos asamazipange play okha ndipati? Ndinali mu Sana madzulo ano ndili pa mzere Olipila paja mix mnapqlanga follow page ya wild lagos zinangofikilatu pa chorus nde kumbuyo kwangaku kunali dona inayake kaya inaona kaya๐Ÿซฉ
1
853
Paja ndikati ndiyankhuleko mutation ndine wa congress, koma moti izizi nzabwino?
People are in pain out here, and DPP leadership is failing miserably this crisis is deeper than we think
1
111
Mukandionera patali ndimaoneka ngati ndine opanda ndalama koma mukandiyandikila ndipomwe mungadziwe kuti ndalamazo ndilibedi๐Ÿซฉ
4
222
Ingompangani follow nkazionera konko
Before I follow, somebody or herself let me know, is this chigoba or really her?
55
Zisakhale kuti amashowanatu chifukwa mu7 sanachenjere mongokumbutsana Samia paja ndi widow
61
Apapa timboleze anyamata a dpp wa zawavuta tisaname
39
Mtima olimbikila tilinawo koma vuto nkobadwira tsopano๐Ÿ˜ฎโ€๐Ÿ’จ
1
2
121
Am with her sikuti poti ndi kholo ndekuti ndi anzeru kuposa iweyo and it's not a must kuti tiziwamvera zilizonse
Kuchikakamiratu chiwalo ๐Ÿ˜‚
44
Munthune ndine owonoka bwino ndithu. Zimangosowekera ndi ndalama kuti zinditsuke ndiwale๐Ÿƒ
49
Cholinga chawo akufuna kudzasokoneza ma demo into riot same zomwe amachita q mcp zija
Kodi mesa anzanu akufuna kupanga ma Demo on the same day? One year in government yakwana mu November ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ
68
Akuti bwana mphande's Facebook page to reach 100k followers in just 1 day has revealed how Malawians mindset is, akuti a Malawi amakonda nkhani zonyengana kusiya zoti zingatukule miyoyo yawo, inu mukuiona bwanji nkhaniyi?
60
Pa msapha sasewewerapo
I was born with HIV, and whenever men find out about my status, they avoid me. But I'm human too. I deserve love, affection, and happiness just like everyone else. It's not my fault I was born with HIV. โค๏ธ
1
75