YONECO FM (@yonecofm) header
YONECO FM (@yonecofm) profile picture

YFM Radio is a youth focused radio for Youth Net and Counselling (YONECO) and was established in October 2014. Call +265882000302 to advertize

Zomba Malawi
Joined July 2015
Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)Photo by YONECO FM (@yonecofm)
MFUTI MUSAMANGOZIWONERA PATALI! TIYENI TIKAWOMBE LIMODZI NDI ASILIKALI ANKHONDO!
1
1
33
#YFMOnline Nyale Institute for Sexual and Reproductive Health Governance executive director Dr. Godfrey Kangaude has vowed to continue advocating for access to safe and lawful abortion in Malawi. By Smart Sochela yonecofm.com/index.php/2026/…
22
#YFMOnline The Tobacco Commission has called on stakeholders in Malawi’s tobacco industry to strengthen efforts to eliminate child labour and ensure that children have access to education. By Alinafe Nyasulu Read more: yonecofm.com/index.php/2026/…
2
24
#YFMOnline Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika waimitsa msonkhano wa nyumba ya malamulo womwe umayenera kuyamba pa 9 November mpaka pa 11 December chaka chino. Wolemba: Betty Byson
1
1
63
M'kalata yomwe alembera sipikala wa nyumba ya malamulo, a Mutharika ati achita izi pofuna kulola boma kuti ligwiritse ntchito ndalama za mkumanowu pothana ndi vuto la ng’amba komanso kusowa kwa mafuta. A Mutharika ati mmalo mwake nyumba ya malamulo idzakumana chaka chamawa.
1
1
31
#YFMOnline Mkulu wa bungwe la CAMA a John Kapito wapempha mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika kuti agwire ntchito limodzi ndi wachiwiri wawo Dr Jane Ansah pofuna kuthetsa mavuto azachuma omwe dziko lino likukumana nawo. Wolemba: Dex Mpando
1
38
M’kalata yomwe a Kapito alembera a Mutharika, ati anthu ambiri osauka m’dziko muno akuvutika kupeza chakudya cha tsiku ndi tsiku, motero akufunika njira zothetsera mavutowa.
1
7
#YFMOnline Katswiri wa zandale a George Phiri ati mtsogoleri wa chipani MCP a Lazarus Chakwera akuyenera kusiya utsogoleri wa chipanichi ndi kuthandizira munthu amene chipanicho chidzasankhe kuti atsogolere, ngati chikufuna kudzapambana chisankho cha chaka cha 2030.
1
1
30
A Phiri ayankhula izi potsatira malipoti akuti a Chakwera akufuna kudzayimiranso MCP pa chisankho chikubwerachi, ngakhale malamulo a chipanichi sakuwalola kutero.
1
6
#YFMOnline Communication practitioners in the country have been challenged to use modern technologies, including Artificial Intelligence (AI), responsibly to avoid damaging their professional reputation. yonecofm.com/index.php/2026/…
1
51
#YFMOnline Malawi Law Commission has completed the development of legislation aimed at protecting whistleblowers and witnesses. yonecofm.com/index.php/2026/…
1
1
2
59
Special Law Commission chairperson, Justice John M. Chirwa said the Commission’s findings and recommendations are contained in a report to be submitted to Justice minister Charles Mhango.
1
23
The Malawi National Women’s Football Team, the Scorchers, will on Friday, October 9 2026, have to bank on their impressive performance at WAFCON to overcome Zimbabwe in the Los Angeles 2028 Olympic Qualifiers in Lilongwe. By Joy Khakona yonecofm.com/.../scorchers-g…
49
#YFMOnline Malawi is recording measles cases at levels far above what is normally expected, with some districts registering more than 400 cases against a threshold of 25 cases per one million children, ministry of health official says.
31
#YFMOnline Bwalo lalikulu la milandu mawa Lachisanu likuyembekezeka kupereka chigamulo pa pempho la belo la omenyera ufulu wa anthu a Sylvester Namiwa. Izi ndi malingana ndi kalata yachidziwitso yomwe woweruza milandu, a Mzonde Mvula, atulutsa. Wolemba: Augustine Muwotcha
1
1
1
59
A Namiwa, omwe ndi mkulu wa bungwe la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives, anamangidwa pafupifupi masabata atatu apitawa ndipo akuimbidwa mlandu wofuna kulanda boma komanso kufalitsa nkhani zabodza zomwe zingayambitse chisokonezo.
8
#YFMOnline Civil Society Elections Integrity Forum chairperson Benedicto Kondowe has expressed disappointment with the Malawi Electoral Commission’s decision to postpone the September 29, 2026 parliamentary by-elections for Nsanje South and Mangochi East constituencies.
1
35
MEC spokesperson Sangwani Mwafulirwa said the Commission had postponed the by-elections because its electoral materials warehouse in Lilongwe remained sealed, affecting preparations for the polls.
11
#YFMOnline PDP president Kondwani Nankhumwa, UTM president Dalitso Kabambe and UDF president Atupele Muluzi have called for the immediate release of detained activist Sylvester Namiwa, who has been charged with treason. By Mayamiko Mwikhoma
1
37
Police IG Richard Luhanga has summoned CDEDI Executive Director Sylvester Namiwa, just hours after Lands Minister Chimwemwe Chipungu demanded an apology over a press briefing in which CDEDI called on the minister to provide evidence on his wealth and financial dealings.
1
2
162
#SportsNews Ntchito yokonza bwalo la zamasewero la Zomba ikupitirirabe pofuna kuti likhale labwino komanso likwaniritse miyezo yoyenera. Wolemba: Yvonne Chambo
1
41
Mneneri wa khonsolo ya mzinda wa Zomba, Aubrey Moses, wati ndalama zomwe khonsoloyi imapeza kuchokera ku masewero a ligi ya FDH Bank Premiership zikugwiritsidwa ntchito kumalizitsa ntchito yomanga zipinda zovalira osewera.
6
Apolisi amanga a Macmillan Mvevula azaka 25 powaganizira kuti akukhuzidwa ndi kuphedwa kwa a Atughanile Chomo omwe anali dokotala pachipatala cha Queen Elizabeth mumzinda wa Blantyre. Wolemba: Peter Davieson
1
102
Wachiwiri kwa wofalitsa nkhani za apolisi a Alfred Chimthere ati oganizilidwayu wapezeka ndi foni yammanja yamtundu wa Redmi yomwe ikuganizilidwa kuti inali ya ophedwayu.
13
#YFMOnline Bungwe la Malawi Revenue Authority (MRA) lakwanitsa kutolera ndalama za misonkho zokwana K20 biliyoni kuposa mlingo womwe linkayembekezera pa miyezi itatu yoyamba ya chaka cha boma. Wolemba: Yvonne Chambo
1
44
Malinga ndi kalata yomwe MRA yatulutsa, bungweli latolera ndalama zokwana K1.398 trilioni kuyambira mwezi wa April mpaka June chaka chino. Ndalamazi zaposa mlingo wa ndalama zokwana K1.378 trilioni zomwe bungweli linapatsidwa kuti likwaniritse mmiyezi itatuyi.
5
#YFMOnline Mabizinesi oposa 20 akuyembekezeka kutenga nawo mbali pa chiwonetsero cha malonda chomwe ndi cha masiku awiri kuyambira pa 26 mpaka 27 June 2026 mumzinda wa Zomba. Wolemba: Yvonne Chambo
1
42
Mtsogoleri wa Zomba Business Fair, a Lipihelani Mkhupera, ati chiwonetserochi, chomwe chikuchitika kachisanu ndi chimodzi, chipereka mwayi kwa amalonda ang'onoang'ono a m'boma la Zomba komanso madera oyandikana nawo kuti awonetse ndi kukweza malonda awo.
1
14
#YFMOnline About 300 young people in Zomba are expected to strengthen their financial independence through increased honey production following a donation of 100 beehives by AGRA, through Emeritus Reinsurance Company. yonecofm.com/index.php/2026/…
2
21
#YFMOnline Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika akuyembekezeka kunyamuka lero kupita mdziko la South Africa pa ulendo wapadera. Mlembi wamkulu wa Boma, a Justin Saidi, ndi amene walengeza za ulendowu. Wolemba: Augustine Muwotcha
29